sholigah - afa ndi mtima lyrics
hook
ndimomwe ndimaimbila fans imandifila…
haaa! fans imandifila nde…
ndimomwe ndimavalira mphasha ndimaisata,
dollar ndimazisaka, zina ndimazimwaza.
olimbana ndi ine, afa ndi mtima.
ofuna kupanga za ine, afa ndi mtima.
ofuna kugwetsa ine adah, afa ndi mtima.
afune asafuna koma afa ndi mtima…
vers1
anawa amaimba koma mmmh adah mu yao.
amatha k-menya single ndikuposa alb-m yao.
pano ndili pa mwamba ngati
pa zoba wina dazi.
ngati muli otentha ndi otcheni (ocean) ngati madzi.
ndili sick, kwambili… nthenda yake yoopysa”
andipeza ndi tb ndafanana ndi josua”
nyimbo zanga ndi psquare zinafika popita (paul, peter).
olimbana ndi sholigah akusowa chochita.
ndili ngati pc naneso ndimazi sata“
chif-kwa ndinatchuka akazi amandisaka.
palibe amandidya koma ine ndiotopa.
ngati sumandidziwa phw-nga iweso ndi zoba.
ambiliwa samatha nde palibe angandigwetse man.
ndimazifila ngati thukuta la yesu mu getsemani“
ndinu makwacha adah,, ndine pound.
zima style ndizambili ndi masintha, ground.
(hook)
vers2
zaine amachonga nike koma ndine all star.
show ya makape sindipezeka pa poster“
ukape sindimatha, mboni yanga ndi yung-z.
creo amadanda coz ndimakonda n-z-.
ndili pamwamba zedi ndizatsikapo ndi patachute.
ndimatchena ndili bare olo nditavala suit.
akazi ofuna ine amangopanya ma cv.
ngati sumandidziwa mphwawi kwanu kulibe tv.
fans imandifila, ndimathokoza jesus.
ndima disser mafana opusa ndikukhalitsa ziii basi.
sholigah ndi mazoba savana (savanna) ngati bawa.
pa gulu lamazoba nde sholigah amatha.
zokuti ndine chiphe aliyese amadziwa,
amene amakuposayo kwaine amadiwa.
ndili ngati zimbabwe naneso ndili pa map.
hip-hop ikhale barcreys
bwezi ndikungotenga ma cup
(hook)
vers3
ma mcees achulukawa ndi
nde sholigah kuimba bwinoku
chif-kwa kuimba bwinoku kwaiye ndi
nde zothoka zopusa mafana pumulani.
ndine chigawenga ndinapachika nkhawa zanga.
ndimapha aliyese kaya anzanga.
ndilibe chibale ndili ngati faith.
ndimakhala ndabanda nde ndikamaika vers.
ndimatha chilichonse kupatula china chake. chimaenda usiku
ndaiwala ndina lake
ambiliwa ndi ma min simomwe amandiopera.
zoti amandiposa sizingamveke or atakasiya pa air -2.
hook
Random Lyrics
- hannah diamond - every night lyrics
- killer mike - cain & abel lyrics
- sleaford mods - the demon lyrics
- logic - soul food lyrics
- aygun kazimova - yar yar lyrics
- lee hong ki - still (as ever) lyrics
- michael stipe - saturn return lyrics
- feeling - safety dance lyrics
- maude - grab lyrics
- maude - eve lyrics