suckle - dzuwa lisanalowe lyrics
intro(hazel & suckle)
yey yeh yeh yeeeh!
hehe..! suckle, is all oh well!
kanyamata kanyamwale
its your boy hazel
verse 1(suckle)
aaa! life yanga ndichi testimony//
kukhala ndi moyo ndichisomo choti//
w-ngondikondera ndine wake mmodzi//
onyozetsa dzina lake you can guess it homie//
koma k-mwamba tikafika//
moyo wamazuzo ku africa//
ongodzadza ndi imfa ndi matenda bruh//
dzuwa lis-n-lowe yesu ndiye yankho man//
mtsogoleri wa ochimwa//
watsogolo lowala koma pano linathima//
nkhani ndikolowera ulendowu ndiwosayima//
okomedwa atsalira ulendowu ndiwamtima//
ima!usavere dziko samala ndipo//
dikira usakhale ndipo dolo wa tchimo//
imfa yake yapantanda ndika daily good news//
pano pride yatipha all the ba’s are fools//
hook(hazel)
lis-n-lowe dzuwa atate ndikufuna(mukhale nane!)
chisomo chanu atate eeeh! (chifike pa ine!)
lis-n-lowe dzuwa atate ndikufuna (mukhale nane!)
chisomo chanu atate ooh! ooo ooh!
.
dzuwa lis-n-lowe eeeeh!(zambiri zimachitika yeh yeh!nkhondo kaduka nsanje iyee!)/
pena ndimadera nkhawaaa(ndimalingalira ndapanga chani chomusangalatsa yahwe dzuwa lis-n-lowe)/
verse 2(suckle)
eya lis-n-lowe pavuta ndi pati//
ndine sin master ndikusaka mwazi//
wake wapantanda unditsuke basi//
h-ll fire simatengera ali ndi dazi//
wayamba ntchito mwa ife sangasiyire pompo//
olo ntakhala wa up town opanda inu local//
inuyo ndima key awamumtima w-nga lock//
mukatseka mu mtima zachikunja zonse nono//
oh god! dzuwa lis-n-lowe ndimasowa mphamvu//
yochita zofuna zanu moyo uli wefuu//
this life is full of mercies life full of grace//
ochimwa olungama onse mtendere amawupeza//
dzuwa lis-n-lowe life yanga nde ndi bomba(bomb)//
simachedwa kuphulika ka mistake ka pompa//
dzuwa lis-n-lowe life yanga nde ndi bomba(bomb) //
simachedwa kuphulika ka mistake ka pompa//
hook(hazel)
lis-n-lowe dzuwa atate ndikufuna(mukhale nane!)
chisomo chanu atate eeeh! (chifike pa ine!)
lis-n-lowe dzuwa atate ndikufuna (mukhale nane!)
chisomo chanu atate ooh! ooo ooh!
.
dzuwa lis-n-lowe eeeeh!(zambiri zimachitika yeh yeh!nkhondo kaduka nsanje iyee!)/
pena ndimadera nkhawaaa(ndimalingalira ndapanga chani chomusangalatsa yahwe dzuwa lis-n-lowe)/
verse 3(hazel)
our father who art in heaven//
hallowed be thy name//
dzuwa lis-n-lowe mukhale nafe//
chotsani kaduka ndi nsanje//
mutipatse zosowa zathu//
bring unity among us god//
dzuwa lis-n-lowe mukhale nafe eee! dzuwa!! //
hook(hazel)
lis-n-lowe dzuwa atate ndikufuna(mukhale nane!)
chisomo chanu atate eeeh! (chifike pa ine!)
lis-n-lowe dzuwa atate ndikufuna (mukhale nane!)
chisomo chanu atate ooh! ooo ooh!
.
dzuwa lis-n-lowe eeeeh!(zambiri zimachitika yeh yeh!nkhondo kaduka nsanje iyee!)/
pena ndimadera nkhawaaa(ndimalingalira ndapanga chani chomusangalatsa yahwe dzuwa lis-n-lowe!)
Random Lyrics
- robot house - miss piggy lyrics
- asimoylen, justray - тест-драйв (test-drive) (intro) lyrics
- valerie - digitally lyrics
- adan - 14 de febrero lyrics
- young maylay - aint official like us lyrics
- la garfield - cómo amarte (versión con charles ans) lyrics
- heavens edge - can't cry anymore lyrics
- monkey business music - stay in school (remix) lyrics
- thor (band) - rosie lyrics
- slight syruse - manicomio lyrics