suckle - intro lyrics
Loading...
ine ndimagona//
kudzuka osalota//
osamanditchula star sindimafuna kuwala chikoka//
ndimayenda ndicholinga pano ndi abraz//
thupili ndi temple mokhala okhetsa mwazi//
mtendere ndikusangalala zokhaso basi//
ayi njee kugawa mawu ndicholinga chathu//
eeh eya ma guy ndinewakhama ngini zanga zimayenda mwa kaya//
sorry ma guy ndilibe chuma koma za dziko nde zimandig#ya//
zimandinyenya zimandiphwanya//
mtima odzadza ndi dama chandichosera ch#nkhwaya//
awo kaya yesu w#nga wauka//
#n#li ndi mwayi oborna ona pano awutaya kupembedza chauta//
chomwe nnakhazikitsa mu mtima mw#nga inu kaya//
checka boldness ase koma suckle ndiwakhama//
ladies and gentlemen!
welcome to sleep without dreams extended playlist!
Random Lyrics
- clairo - 4ever remix lyrics
- kino (lgdg) - kino freestyle 1 lyrics
- the j. geils band - chimes lyrics
- kira spirandelli - não pode parar lyrics
- evan olson - manhattan lyrics
- evan olson - tin man lyrics
- absolut-p - the 1'z lyrics
- yot club - comfort zone lyrics
- chaton - le flambeau lyrics
- sea sic - you already kno lyrics