suffix (mwi) - kwanu nkwanu lyrics
[intro:]
listen
[verse 1:]
bambo anga ankandikhazika
pansi, ndili mwana wovuta
ndili chakusekondale heee ndisakuganizaso zoyimba
mwana w+nga ndithu kukula
ife taonapo yambili mvula
ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu k+manda
kusukulu komwe uliko, uzik+mbuka komwe uchokela
nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe +n+lowela
[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w+nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w+nga
dziwa dziwa mwana w+nga
dziwa dziwa, mwana w+nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga
heeehhh
[post+chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[verse 2:]
yea, life sikhala fair
macritisism sabweletsa sheda
aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela
k+masiyanitsa azako ndiabale
ena utavutika sangathandize m’bale
osamatengeka akamakuchemelera
enawo ukazazizila azakupanga chandamaleee
[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w+nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w+nga
dziwa dziwa mwana w+nga
dziwa dziwa, mwana w+nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga
heeehhh
[post+chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[outro:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w+nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w+nga
dziwa dziwa mwana w+nga
dziwa dziwa, mwana w+nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu
mwana w+nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w+nga
heeehhh
Random Lyrics
- rattlesnakes - hey mother lyrics
- necra - ragnarök lyrics
- young dannyboy - changed lyrics
- superox - hold me close lyrics
- beauty school - astel lyrics
- pasteur papillon - ce qui ne tue pas lyrics
- mezozoy - фарамант (faramant) lyrics
- von seiten der gemeinde - ritterschlåg lyrics
- garden graves - blood and steel lyrics
- an'om - subtil lyrics