teddy - desperate lyrics
m’ma
makadidido eeh
oh yeah, oh yeah, ooh yeah
i know it’s not okay
kuti nthawi zonse nzikukulonda iwe
baby i can’t help it
i still belive the odds will play in my favour
do you think of me
olo mwina zoyi ndakusowa iweyo
nthawi yonseyi
nd+nkaganiza zoti sungagwidwe
kapena mwina m’minyama (aaah)
zoti unandithawa (aah)
pano yatsala ndi nkhawa (aah)
iwe sunkandikonda (aah)
kodi unandinamiza? (aah)
when you told me love always wins
ine ndimanva kuwawa
daily nkama ku stalker (and)
i know it’s not okay
it’s not okay
it’s not okay
it’s not okay
baby i am desperate
i am desperate
i am desperate
i am desperate
ma ine, ma ine
daily m’mangoganiza za iwe
anzanga nawo amathoka za iwe
anzako nawo akuti you’re happy iwe
nn+z+yambilanji za chikondi izi?
zanga zimangothela misonzi
why do you look better and excited?
zaka zonsezi sunawonekepo chonchi iwe
kapena mwina m’minyama (aaah)
zoti unandithawa (aah)
pano yatsala ndi nkhawa (aah)
iwe sunkandikonda (aah)
kodi unandinamiza? (aah)
when you told me love always wins
ine ndimanva kuwawa
daily nkama ku stalker (and)
i know it’s not okay
it’s not okay
it’s not okay
it’s not okay
baby i am desperate
i am desperate
i am desperate
i am desperate
kapena mwina m’minyama (aaah)
zoti unandithawa (aah)
pano yatsala ndi nkhawa (aah)
iwe sunkandikonda (aah)
kodi unandinamiza? (aah)
when you told me love always wins
ine ndimanva kuwawa
daily nkama ku stalker (and)
Random Lyrics
- the fixx - saved by zero - live (canada) lyrics
- mursia - no me olvido lyrics
- urban cafe crew - you bring love to life lyrics
- nastee chapel - the bucket lyrics
- kittib - 좋겠다 (i wish) lyrics
- bill nuggens - наруто lyrics
- addy faith - so does she lyrics
- basshunter - i miss you (fonzerelli edit) lyrics
- iiamchiz - don’t waste my time lyrics
- yun mufasa - 100 verses lyrics