trappy beats & fada moti - weekend lyrics
[intro : fada moti]
aseh trappy!
eh!
eh!
eh! eh!
internationally ting say
eh!
[chorus: trappy beats & fada moti]
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye)
[verse 1:fada moti]
motily moti
tifela weekend musabalalike
lerolo bayala alire
asanafike adabwitsike payende mowa ngati mtsinje
tifela weekend musabalalike
lerolo bayala alire
asanafike adabwitsike payende mowa ngati mtsinje
[refrain: fada moti]
wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
iwe tadekha umbombo taleka leka
wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
iwe tadekha umbombo taleka leka
[pre+chorus: trappy beats]
adekhe (masese)
adekhe (masese)
adekhe (masese)
adekhe (masese)
adekhe (masese)
[chorus: trappy beats & fada moti]
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye) (adekhe masese)
[verse 2: trappy beats]
dziko lonse kwakoma ndikuno
dziko lonse pakoma ndipano
fada wa vunga plan
lero tiichemesadi
aliyense azipanga zake
maluziwo isandipake, poti
[refrain: fada moti]
wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
iwe tadekha umbombo taleka leka
wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
iwe tadekha umbombo taleka leka
wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
iwe tadekha umbombo taleka leka
wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
iwe tadekha umbombo taleka leka
[pre+chorus: trappy beats]
adekhe (masese)
adekhe (masese)
adekhe (masese)
adekhe (masese)
adekhe (masese)
[chorus: trappy beats & fada moti]
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye)
tifela weekend (aah aye) (adekhe masese)
Random Lyrics
- 4d4m - get you off my mind lyrics
- gravity stone - ascent - live lyrics
- sezer sarıgöz - bakma bana öyle lyrics
- con funk shun - sure feels good to me lyrics
- sal houdini - my valentine lyrics
- harpo - the world is a circus lyrics
- yolyboy - oluwa bless me lyrics
- big yba - 30 lyrics
- mickey diamond & big ghost ltd - reggiani's revenge lyrics
- the last dinner party - godzilla lyrics