twnda - zimvekemveke lyrics
[intro: shano index]
brain bang+bang inna mi head
shano
[chorus: twnda]
ndinene motani? (ndinene motani?)
kuti zimveke mveke mveke mveke mveke
ndinene motani?
kuti zimveke mveke mveke mveke mveke
kuti zimveke eeeeh
kapena ndikuwe?
kuti zimveke, kuti zimveke eeeh
kapena ndikuwe?
kuti zimveke
[verse 1: twnda]
moni ku stand, muli bho? muli njibwa?
ndabwera ndi ka ninkha
mwina mwakamva kale, uh+huh
msungwana wokondedwa
amakhala ‘fupi n’pa chipeta paja
wandipasa katheka
mtima mwake zatheka
[pre+chorus: twnda]
chikondi changa chi, chopanda malire
sindingatsinzine, sindingaphethile
tatenga nkono w+nga, ndiyandikire
ndi zathu zonse izizi
[chorus: twnda]
ndinene motani? (ndinene motani?)
kuti zimveke mveke mveke mveke mveke
ndinene motani?
kuti zimveke mveke mveke mveke mveke
kuti zimveke eeeeh
kapena ndikuwe?
kuti zimveke, kuti zimveke eeeh
kapena ndikuwe?
kuti zimveke
[verse 2: shano index]
me and my friend tinamvelapo story
i know you’re busy but i’m not fine
nkhani inkamveka ija pano pali namwali w+nga
ndunena pano n’funa ndimveke velo yo, uh+huh
muzabwere, ah
everyday iye m’maso mwa ine
dzuwa likatuluka ndimawona iye
anakonda ine, ine n’nakonda iye
pena ntima umagunda, umagundila iye
[pre+chorus: shano index]
chikondi changa ndi chopanda malire
sindingasinzine, sindingaphethile
tatenga nkono w+nga
ndi zathu zonse izizi
[chorus: twnda & shano index]
ndinene motani? (ndinene motani? nene motani?)
kuti zimveke mveke mveke mveke mveke
ndinene motani? (motani? ah)
kuti zimveke mveke mveke mveke mveke
kuti zimveke eeeeh
kapena ndikuwe?
kuti zimveke, kuti zimveke eeeh (zimveke)
kapena ndikuwe?
kuti zimveke
Random Lyrics
- uliana royce - не твоя (i'm not yours) lyrics
- vámosi jános - ha ősszel lyrics
- your broken hero - fantasy lyrics
- the slime prophet - light in the darkness lyrics
- lida husik - do me right lyrics
- blood force trauma - 1312 lyrics
- error (deu) - millers planet lyrics
- barış diri & gülşen karanlık - şimdi sen lyrics
- dizzyeight - war with me lyrics
- spiegel (rapper) - romona flowers lyrics