azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

xi (mw) - kudzanjoya lyrics

Loading...

[intro]
pr+nex

[pre+chorus]
ife tinasiya k+mwa
koma lero tiledzera ndi fanta lomweli
achina kayo akafika awuze
atipeza kuseli
yo, these chicks are h+lla classy here
zikukhangati athawira kugeli
kunyumba asiya babe
koma akachoka kuno?
azichoka ndi ma baby (xi)

[chorus]
kuno ndabwera kudzanjoya (ah iwe), kudzanjoya (woo)
kuno ndabwera kudzanjoya (ay, ay, ay)
kudzanjoya (uh+huh, uh+huh)
kuno ndabwera kudza, yeah (kudza?), kudzanjoya
kuno ndabwera kudzanjoya (uh+huh, eh), kudzanjoya (woo)

[verse]
kuno ndabwera kudzanjoya
minding my own business
i’m sipping on coca+cola
chitumbuka timathaso, mamie
muli makora? (muli makora?)
whether you’re a drunkie or whether you’re a stoner
tangofikani kuno man
tonse tidzanjoye
yeah, tili ku open air ya poly
“don’t you learn at mzuni”
girl, today, i learn at poly
she offеred me some breezеr
i told her i was cool
but if i’m to tell the truth
[pre+chorus]
ife tinasiya k+mwa
koma lero tiledzera ndi fanta lomweli (fanta lomweli)
achina kayo akafika awuze
atipeza kuseli (atipeza kuseli)
these chicks are h+lla classy here
zikukhangati athawira kugeli (athawira kugeli)
kunyumba asiya babe
koma akachoka kuno?
azichoka ndi ma baby (xi)

[chorus]
kuno ndabwera kudzanjoya (ah iwe), kudzanjoya (woo)
kuno ndabwera kudzanjoya (ay, ay, ay, ndabwera kudzanjoya)
kudzanjoya (uh+huh, uh+huh)
kuno ndabwera kudza, yeah (kudza?), kudzanjoya
kuno ndabwera kudzanjoya, kudzanjoya (woo)



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...