azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

yobezani - ndikuyamika lyrics

Loading...

[intro]
classic!
mmm+mm… orama!
yobezani
eeeh!
emmanuel, yeah!

[verse 1: orama]
eeeh! akandiwona
n’takhumudwa n’sakukondwa
k+makondwera iwowa
k+mandijeda iwowa
eeeh! mbuye w+nga ndi mtondo, ndi mtondo, ndi mtondo
tate w+nga ndi leader, ndi leader, ndi leader
tate w+nga ndi leader
ndipo sindidzalira
ndithu sadzandisiya
ine ndikuyamika!

[chorus: orama]
yeah, i gotta be honest
siwina koma inuyo
sin’zitengera chizolowezi
i owe it all to you, lord!
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
[verse 2: yobezani]
ndilibe chif+kwa chodzitamira
‘cause i know i’m just a product of your grace
chipanda inu bwezi nditataika
no doubt, yeah i coulda been some waste
n’nalawa ubwino wanu
munandigula ndi mwazi n’kundipanga wanu
munandipatsa moyo wina, now i’m brand new
and i’m enjoying its fullness, sorry dan lu
yeah! i acknowledge it’s all you, lord
m’mene n’nali mu dead+end munali clue, lord
ndikupanga sеlf+searching munali google
till i found myself еngulfed in your cool love
ngiyabonga!

[chorus: orama]
yeah, i gotta be honest
siwina koma inuyo
sin’zitengera chizolowezi
i owe it all to you, lord!
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika

[verse 3: emmanuel]
kundiombola m’zikh0m+
adani anatseka, mwanditsegulira kh0m+
nkhawa n’napachika ndimayenda mu zisomo
ndi yesu zonse zinayera n’mwazi osati omo
zomwe mwachita pa moyo w+nga indedi n’zambirimbiri
mwakuza malire anga, ndikundisinthanso mbiri
adani kundipinga n’cholinga choti andikole mu goli
koma munandi+saver m’manja mwawo, munawayika zigoli (haha!)
ndadza pano kunena zikomo
mdalitso wanu umabweretsa bata m’timamo
sindikulabada olo dyabu akoke tsinya
chomwe ndikuchita nkhumupokela chiuta wa ku chanya
[chorus: orama]
yeah, i gotta be honest
siwina koma inuyo
sin’zitengera chizolowezi
i owe it all to you, lord!
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika
yamika, ndikuyamika



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...