![azlyrics.biz](https://azlyrics.biz/assets/logo.png)
zeze kingston & leumas - mphaka lyrics
[intro]
ayy, y’all, tiyeni
tiyeni, tiyeni, tiyeni
[hook]
wadzuka bwanji neba, ndiwe wobhebha
ufunika mamuna woti zake zikuyenda
kamamuna kawo kakhoza kuyenda
chabwino katsale ‘f+kwa akhoza kugenda
heh, koma akangosuntha ndizibwera kwanu kudzafuntha
ine ndi mfana wanjalatu, ndidzibwera kwanu kudzakhuta
[chorus]
cristina
(mphaka wachoka, makoswe atase)
kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
iwe si nsima
(mphaka wachoka, makoswe atase)
kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
iwe si nsima
(mphaka wachoka, makoswe atase)
kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
[verse]
ndapeza muti athira mu milo
athira mu milo
bread mpakana ma peace four
mpakana ma peace four
mowa w+nga andimwera
ndapeza mowa w+nga andimwera
ndatsegula mu fridge mw+nga ndi chi+confidence
nyama yonse andidyera
ndapeza muti athira mu milo
athira mu milo
bread mpakana ma peace four
mpakana ma peace four
mowa w+nga andimwera
ndapeza mowa w+nga andimwera
ndatsegula mu fridge mw+nga ndi chi+confidence
nyama yonse andidyera
[hook]
wadzuka bwanji neba, ndiwe wobhebha
ufunika mamuna woti zake zikuyenda
kamamuna kawo kakhoza kuyenda
chabwino katsale ‘f+kwa akhoza kugenda
heh, koma akangosuntha ndizibwera kwanu kudzafuntha
ine ndi mfana wanjalatu, ndidzibwera kwanu kudzakhuta
[chorus]
cristina
(mphaka wachoka, makoswe atase)
kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
iwe si nsima
(mphaka wachoka, makoswe atase)
kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
(mphaka wachoka, makoswe atase)
(mphaka wachoka, makoswe atase)
[verse]
ndapeza muti athira mu milo
athira mu milo
bread mpakana ma peace four
mpakana ma peace four
mowa w+nga andimwera
ndapeza mowa w+nga andimwera
ndatsegula mu fridge mw+nga ndi chi+confidence
nyama yonse andidyera
ndapeza muti athira mu milo
athira mu milo
bread mpakana ma peace four
mpakana ma peace four
mowa w+nga andimwera
ndapeza mowa w+nga andimwera
ndatsegula mu fridge mw+nga ndi chi+confidence
nyama yonse andidyera
[outro]
mpaka, mpaka, mpaka, mpaka
ayi, yah+yah+yah
ayi, yah+yah+yah, yah+yah
ayi, yah+yah, yah+yah+yah
makoswe atase
ayi, yah+yah+yah, eish
tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni
tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni
ah+yeah+yeah
Random Lyrics
- babak behnam - gözlərin aladır, yar lyrics
- coach k - slopes lyrics
- sefa - bach met discobal lyrics
- xluno - incase i never see you again lyrics
- vega7 the ronin - akai pads lyrics
- amer - lit lyrics
- peacemaker fl - five ways to hide a dead body lyrics
- literalhat - tomorrow lyrics
- lipstick (nz) - nightmare on elm street lyrics
- kaseis - diluvio lyrics