azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings – mwana uyu lyrics

Loading...

verse 1 (kelvin sings)

monga mwana w-ng’ono amadalila kholo
kutsala yekha amakanitsitsa toto
saayenda yekha angakagwele k-mphopho
kusangalatsa namalengaso ndi choncho

osati matukutuku
ngati ukukankha chikuku
pamaso pamunthu w-nkulu
osadutsa mukusuta ndudu

chisomo chake ndichokwanila tonsefe
chitsanzo ndi mwana wa maria ndi yosefe
pofunika mtanda wake tiwusenze
chomwechi mpakana k-malembe

poti iye ndi syllabus
timulonde mapazi
tisachite manyazi
akationa nk-mati

chorus

mwana uyu uyu uyu
mwana uyu uyu uyu
ndiw-nga aaa
ndiw-nga aaaa

bridge

ndifuna akandiona ine
a-zi-ti
mwanayu ngw-nga ine
nde chitsanzo ndi nsembe
you’d think that he’s a lannister
the way he paid my debt!!
nde chili kwaine kufalitsa
eeehe
zachozizwa chomwe wachita
eeehe
nde kulikonse komwe nzapita
i’ll represent christ to the fullest wazizur?!!

verse 2 (suffix)

yeah!!
ambuye anati mfana wopanda ntchito you need some company
mu aiguputo si mo salah upite canaan
ndipo, ankadziwa ndani mwala okanidwa uzabuilder mfana ankakugendani

posamila panga
chitsime cha kuya koma posamila phw-nga
okontrola madzi mpaka osamila nkhw-ngwa
kusintha mfana wa magazi othamanga kuposa mira mpaka

timakuwa abba father
amandipasa ma khatcha ndikayamba kudya machaka
love yake jenuwini yosadyesana chi banzi
ine chimwemwe kutsaya nthawi zonse akamati

chorus

mwana uyu uyu uyu
mwana uyu uyu uyu
ndiw-nga aaa
ndiw-nga aaaa



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...