azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

langwan piksy – unamata lyrics

Loading...

verse one
k-mata k-mata ndi superglue
uli duu
kuutolatola mtima w-nga pansi uli mbuu
k-mata ndi bostic
mbali zonse kuchta stick
2getha wambawamba osamvetsa yako logic
unali w-nga driver
so loyal to me sunasamale nkhan zomwe un-z-mva
kundimatilira maso ako pa future
kunali chi mdima koma unkadziwa kucha.
kundisekerera
nkamazima kupemelera
moyenera
kundinyengelera mpaka ntakolera
sizinkabisika nanenso nd-nkahopela
koma kugwa muchkondi simmene nd-nkaopela.
ngati kabebe unandilera.
ikamagwa mvula unali umblera.
zomwe unamatazi sizingatheke k-matula.
chikondi chako ndalama sizingathe kugula.

chorus
unatola mtima w-nga uli wosweka, ulibe mantha
mmene ena anaseka, nati ndatheka unanditsata
unamata-mata-mata-mata-mata-mata mtima w-nga
mtima w-nga unawina
sindingampatse wina

verse two
yako fandum
ngat yochita kupanga zoom
ndikondwa mudzi wako onseu ndine mfumu
unamatamatako konse sunasiye room
ena k-mayesera kuti alowe koma hmmm?
ndimakondwera ndikamaona ka view.
nde iweyo ameneyo everyday u look brand new
ndichikondi chako chomwe chindipatsa mphamvu
zonsezi in one sentence honey i love you
kukusiya iwe ndikuluza timing
poti munyengo yaziphaliwali u stood by me
in so doing unawina chikondi cha ine
mpaka muyaya ndiri nawe n’patse poti nsaine.
unakhulupira mwa ine kuchoka pa chyambi
ndisanapsetsetse ndik-mveka khambi.
pano ndapsano umveno ku-kukoma kwa changachi
chikondi
udzingopanga download.

chorus
unatola mtima w-nga uli wosweka, ulibe mantha
mmene ena anaseka, nati ndatheka unanditsata
unamata-mata-mata-mata-mata-mata mtima w-nga
mtima w-nga unawina
sindingampatse wina

verse three
mu mvula ya ziphaliwaliwali unandikonda more
k-mangofeela warm – k-mangofeela bho
kuthamangitsa zinthu zanga zikamayenda slow
k-mangofeela bho – k-mangofeela bho
si inenso wamanyazi sweetie you make me stand tall
k-mangofeela bho – ine k-mangofeela bho
usiku usanagone kundimenyera ka call
k-mangofeela bho – k-mangofeela bho

chorus
unatola mtima w-nga uli wosweka, ulibe mantha
mmene ena anaseka, nati ndatheka unanditsata
unamata-mata-mata-mata-mata-mata mtima w-nga
mtima w-nga unawina
sindingampatse wina



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...