azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lawi – chifundo nane lyrics

Loading...

[intro]
ayy
chifundo nane
chifundo nane
oh, chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
mtima w+nga don’t you worry
everything is gonna be alright

[chorus]
ambuye ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
mtima w+nga sudera nkhawa
chif+kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w+nga sudera nkhawa (oh no)
chif+kwa ali ndi chifundo nane

[verse 1]
machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo
mutazindikira zamumtima mw+nga mukhoza k+mandisala
m+th+ kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m’ndende
ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa
ndiye amene anandipanga amandidziwa
zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika
koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe
amatsegura manja ake ndi kundik+mbatira
[chorus]
oh, ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nanе
mtima w+nga sudera nkhawa
chif+kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w+nga sudera nkhawa (oh no)
chif+kwa ali ndi chifundo nanе (oh, yeah)

[verse 2]
ayi+yayi+yayi
ayi, ndachoka kutali, moyo w+nga ndi umboni
wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete
pomwe adani anga andik+mbira mitsinje
wandimangira mlatho, ndayenda powuma
wandifewetsera zolimba zanga

[chorus]
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ine mtima w+nga (sudera nkhawa chif+kwa ali ndi chifundo nane)
ine mtima w+nga (sudera nkhawa
chif+kwa ali ndi chifundo nane)



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...