azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lulu & mathumela band – ndileke lyrics

Loading...

[verse 1]
pomwe ndikufunitsitsa ndipamene wandisiya
ulibe nazo ntchito olo ntagwera mutu
suk+mva za munthu
koma ine wandisiya ndi ludzu
ndimafunabe pang’ono
pang’ono nk+makuphuzira

[refrain]
darlie tulo [?]
wandikhapila kosathwa
komano ndayesetsa ndafika potopa
ati sudzasiya kundikonda, k+mawuza anthu ena
tsono ngati umandikonda bwanji suli ndine?
tsono taleka ndikuwuze

[pre+chorus]
ndinakupilira mu nzinthu zambiri
zina zoyipa ndimamva titasiyana
koma ukati ulile bodza
uwonetsa kankhope ka m’ngelo
anzako ena ankandifunsiraso
ndilibe chipongwe chabe nd+nkakana
koma ukati undiyalutse anzako akuwona

[chorus]
basi
oh, basi ndileke
basi
oh, basi ndileke
[verse 2]
ngakhale pandekha osandilankhula (no)
ukakhalakhala osafusa za ine (no)
ukamagona usalote ine
(enough is enough, ine ndatopa)
unandichotsa mtima kuyika mwala
pano onse ondiwuza amandikonda
nkaw+ng’ana ndikulira
unandichotsera umunthu w+nga
tsiku osatha ndilire, ndilire, ndilire

[refrain]
ati sudzasiya kundikonda, k+mawuza anthu ena
tsono ngati umandikonda bwanji suli ndine?
tsono taleka ndikuwuze

[pre+chorus]
ndinakupilira mu nzinthu zambiri
zina zoyipa ndimamva titasiyana
koma ukati ulile bodza
uwonetsa kankhope ka m’ngelo
anzako ena ankandifunsiraso
ndilibe chipongwe chabe nd+nkakana
koma ukati undiyalutse anzako akuwona

[chorus]
basi
oh, basi ndileke
basi
oh, basi ndileke
basi
oh, basi ndileke
basi
oh, basi ndileke



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...