national anthem - malawi native anthem text lyrics
Loading...
1.
mlungu dalitsani malawi,
mumsunge m’mtendere.
gonjetsani adani onse,
njala, nthenda, nsanje.
lunzitsani mitima yathu,
kuti tisaope.
mdalitse mtsogo leri na fe,
ndi mai malawi.
2.
malawi ndziko lokongola,
la chonde ndi ufulu,
nyanja ndi mphepo ya m’mapiri,
ndithudi tadala.
zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,
n’mphatso zaulere.
nkhalango, madambo abwino.
ngwokoma malawi.
3.
o! ufulu tigwirizane,
kukweza malawi.
ndi chikondi, khama, k-mvera,
timutumikire.
pa nkhondo nkana pa mtendere,
cholinga n’chimodzi.
mai, bambo, tidzipereke,
pokweza malawi.
sent by carlos andré pereira da silva branco
Random Lyrics
- national anthem - trinidad & tobago anthem text lyrics
- national anthem - turkey anthem text lyrics
- national anthem - tonga native anthem text lyrics
- national anthem - tanzania anthem text lyrics
- national anthem - suriname anthem text lyrics
- national anthem - suriname native anthem text lyrics
- national anthem - sri lanka anthem text lyrics
- national anthem - south africa anthem text lyrics
- national anthem - slovakia native anthem text lyrics
- national anthem - singapore anthem text lyrics