azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

national anthem – malawi native anthem text lyrics

Loading...

1.
mlungu dalitsani malawi,
mumsunge m’mtendere.
gonjetsani adani onse,
njala, nthenda, nsanje.
lunzitsani mitima yathu,
kuti tisaope.
mdalitse mtsogo leri na fe,
ndi mai malawi.
2.
malawi ndziko lokongola,
la chonde ndi ufulu,
nyanja ndi mphepo ya m’mapiri,
ndithudi tadala.
zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,
n’mphatso zaulere.
nkhalango, madambo abwino.
ngwokoma malawi.
3.
o! ufulu tigwirizane,
kukweza malawi.
ndi chikondi, khama, k-mvera,
timutumikire.
pa nkhondo nkana pa mtendere,
cholinga n’chimodzi.
mai, bambo, tidzipereke,
pokweza malawi.
sent by carlos andré pereira da silva branco



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...