ndinezulu – udani lyrics
kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w+nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w+nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala
mwina ndi nyanga zomwe wina ana panga
kapena sinyanga nakuba kapena chabe nikaduka
kamene kalengesa banthu bamozi kupeza vif+kwa
cif+kwa mayeso fufuza koma sina peze cif+kwa eh
kunjako nko kudha macita mantha ndi khalidwe yawa
udani waconco wacoka kuti ma lankhulana
pempelo yanga niyoti izozo ma lalilane
nanga cikondi munali naco cinapita kuti
funso
kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w+nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w+nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala
k+makhalila midesu
ena akulila yesu
mundisamalile ana banja isa pwasuke tikhale ifeso
ogwilizana despite what we facing i hope we don’t break us ineo
pemphelo yanga ndiyoti udani ulipo kuntima uthepo
koma zukhala nga e sizotheka anthuwa afuna afepo
udani waconco ku opya ambuye k+mwamba muyanganilepo
k+ma kangana pa zopanda phindu poka poka ena afepo
anthu wa ndani aloza umbuli wa conci ine sina onepo
kudabwa
nthawi zina ndima dabwa
w+nga anthu momwe ama khala
kubaba mtima w+nga uma baba
ubaba anthu zomwe ama panga
kudana anthu awa ama dana
sibanja ine mango khala
Random Lyrics
- hillsong young & free – everything i could want (live) lyrics
- wise manson – mass appeal lyrics
- outhr – numb for you (outro) lyrics
- spazio unito – la voglia di stare insieme lyrics
- stephen william cornish & amanda leigh wilson – tell me you’ll never leave lyrics
- gridd – three figures lyrics
- scott wesley brown – the lord who loves us all lyrics
- jonathan grinton – clearly (ft. casey may) lyrics
- tram 11 – eto šta ima!? lyrics
- plk – chandon et moët lyrics