azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

sevenomore (mw) – pogona lyrics

Loading...

[intro]
yah
oh+yah+yah
oh+yah+yah
oh+yah+yah
oh+yah+yah

[chorus]
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona, gona
kunkonda pogona
amandifuna pogona, gona
kunfuna pogona

[verse]
k+mbali amandikana, amati ine ndine hule
k+mbali amandinyoza, ati ndine osauka
k+mbali amandikana, amangoti ndine mzake
k+mbali amandinyoza, ati ndimankakamila
koma zikamuvuta amabwera kwathu, “baby ine ndakusowa”
koma zikamuvuta amabwera kwathu, “baby ndili nawe nkhani”
komatu sakamba ayi, amangokhala pa easy
komatu sa+talker ayi, ndimangodziwa ma pg
ndimalakalaka nditabweza chipongwe koma ine zimandikanika
ndimalakalaka nditabweza choyipa koma ine zimandikanika
ndimamukonda ine, sindifuna atandisiya
ndimamufila ine, sindifuna ntamusiya
[chorus]
komabe, amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona
amandifuna pogona
amandikonda pogona, gona
kunkonda pogona
amandifuna pogona, gona
kunfuna pogona

[outro]
yah+yah, yah+yah
yah+yah, yah+yah
yah+yah, yah+yah
yah+yah, yah+yah, prr



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...