the very best – nsokoto lyrics
k-msokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa
kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako
mwana apate eti tiona ngati agone
k-msokoto kuli mfiti imodzi inkalodza ana osalakwa
kupata kwa ana iyo sinkasangalatsidwa nako
mwana apate eti tiona ngati agone
chaka chino chokha iye akagonera k-manda
m’mati n’kwere ndakwera panyumba yanthakati
wakoma bana pawaka
wamara bana nsokoto
mwana akangoti agone
k-m’bwerera usiku
thupi lonse lamangika
kulephera kufuula
poti adsuke mam’mawa
thupi kunjenjemera
mutu w-nga, malungo, matenda aja akula
wakoma bana
wati kitasha
wamara bana
ichi n’chasoni
nsokoto nsokoto
nsokoto nsokoto
muuze nthakatiyo namulondola ife takana
bana bakunsokoto ise
bana bak-mulowe ise
bana bamwakisulu ise
bana bakaronga ise
bana bakurumphi ise
bana bakuchitipa ise
Random Lyrics
- quincy (french) – eclipse lyrics
- bustamante – rezaría lyrics
- social anxiety – falling out of love in the key of d minor lyrics
- famous dex – my gang lyrics
- jordin sparks – 11:11 lyrics
- callejon – vergissmeinnnicht lyrics
- ¡mayday x murs! – my own parade lyrics
- black portland – florida water lyrics
- nectar gang – medusa lyrics
- black kent – bart simpson lyrics